Bambo wa njinga ya moto* (Motorman)
Amakonda kuzungulira ndi njinga yake ya moto, ine
sindimadziwa kuti chikunchitikira nchiyani m’maganizo
ake.
Tsiku lina ndina mutsatira kukanyumba yake ku M’khalango.
Ndinayenda mpaka pakanyumbapo ndikukakha, chitseko
chake nkutsekula.
Nditatsekula ndinawona m’bambo wa njinga yamoto
uja atagona chafufumimba pamitengo pansi.
Anadzidzimuka ndikuyimilira akundi yan’ganitsitsa
mwachidwi ndi nkhope yodabwa.
Ndinkafuna kulankhula naye koma ndisanatelo bambo
wa njinga ya motoyo anasowa osabwerelanso.
Ndinalowa
m’nyumbamo momwe ndinakhazikika kwa zaka makumi
awiri.
Mawuwa ndiwowonadi: Nyumba yatsopano ndiyabwino
kusiyana ndiyakale.
Translation: Tosh Malunga, Senga Bay
*
Chichewa is the main language of Malawi. 'Bambo
wa njinga ya moto' literally means 'Man with bike
of fire' / 'Man met fiets van vuur'.
>>Klik
hier voor het radioverhaal dat Nyk maakte voor
het Vpro-programma Cantina
over
zijn verblijf in Malawi.
©nykdevries 2010
|